Exodus 35:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo atsogoleri adabwera ndi miyala ya onikisi ndi miyala ina yoika pa chovala cha efodi ndiponso pa chovala chapachifuwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi akulu anabwera nayo miyala yasohamu, ndi miyala yoti aiike kuefodi, ndi kuchapachifuwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atsogoleri anabweretsa miyala ya onikisi ndi miyala yokongola yoyika pa efodi ndi chovala chapachifuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi akuru anabwera nayo miyala yasohamu, ndi miyala yoti aiike kuefodi, ndi kucapacifuwa;