Exodus 35:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Mose adauza Aisraele kuti, “Chauta wasankhula Bezalele, mwana wa Uri, mdzukulu wa Huri, wa fuko la Yuda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anati kwa ana a Israele, Taonani, Yehova anaitana, ndi kumtchula dzina lake, Bezalele, mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa fuko la Yuda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Mose anati kwa Aisraeli, “Taonani, Yehova wasankha Bezaleli mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa fuko la Yuda,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anati kwa ana a Israyeli, Taonani, Yehova anaitana, ndi kumchula dzina lace, Bezaleli, mwana wa Uri, mwana wa Huri, wa pfuko la Yuda;