Exodus 35:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta wadzaza Bezaleleyo ndi mzimu wa Mulungu, kotero kuti ali ndi luso ndi nzeru, ndiponso ndi wodziŵa ntchito zonse zaluso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anamdzaza ndi mzimu wa Mulungu, ndi luso, ndi nzeru, ndi chidziwitso, za m'ntchito zilizonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo wamudzaza ndi Mzimu wa Mulungu kotero kuti ali ndi luso ndi nzeru zomvetsa zinthu, ndipo akudziwa bwino ntchito zonse zamanja monga izi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anamdzaza ndi mzimu wa Mulungu, ndi luso, ndi nzeru, ndi cidziwitso, za m'nchito ziri zonse;