Exodus 35:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amadziŵanso kulemba mapulani a ntchito zaluso ndi kugwira ntchito ndi golide, siliva ndi mkuŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kulingirira ntchito zaluso, kuchita ndi golide, ndi siliva, ndi mkuwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulemba ndondomeko ya ntchito zaluso ndi kupanga zinthu zagolide, zasiliva ndi zamkuwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kulingirira nchito zaluso, kucita ndi golidi, ndi siliva, ndi mkuwa;