Exodus 35:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amadziŵa kusema miyala yakongoletsera, kujoba matabwa, ndi kuchita ntchito zonse zaluso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kuzokota miyala yoikika, ndi kuzokota mitengo, kuchita m'ntchito zilizonse zaluso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kusema ndi kuyika miyala yokongola, kukonza zinthu zamatabwa ndiponso kugwira ntchito ina iliyonse yamanja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kuzokota miyala voikika, ndi kuzokota mitengo, kucita m'nchito ziri zonse zaluso.