Exodus 35:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Chauta wapatsa nzeru kwa iyeyo ndi kwa Oholiyabu mwana wa Ahisamaki, wa fuko la Dani, kuti aziphunzitsa ena luso laolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaika m'mtima mwake kuti alangize ena, iye ndi Oholiyabu mwana wa Ahisamaki, wa fuko la Dani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Iye wapereka kwa Bezaleli pamodzi ndi Oholiabu mwana wa Ahisamaki, wa fuko la Dani luso lophunzitsa ena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaika m'mtima mwace kuti alangize ena, iye ndi Aholiabu mwana wa Ahisama, wa pfuko la Dani.