Exodus 35:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
thonje lobiriŵira, lofiirira ndi lofiira. Azibweranso ndi nsalu yokoma yabafuta, nsalu zopangidwa ndi ubweya wambuzi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ndi ubweya wa mbuzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nsalu zobiriwira, zapepo, zofiira, nsalu zofewa; ubweya wambuzi;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
golidi, ndi siliva, ndi mkuwa; ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ndi ubweya wa mbuzi;