Exodus 35:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chikopa chankhosa chonyika mu utoto wofiira, zikopa zambuzi, matabwa a mtengo wa kasiya,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wakasiya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zikopa za nkhosa zazimuna za utoto wofiira ndi zikopa za akatumbu; matabwa amtengo wa mkesha,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi zikopa za nkhosa zamphongo zonika zofiira, ndi zikopa za akatumbu, ndi mtengo wasitimu;