Exodus 36:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adasoka nsalu khumi ndi imodzi za ubweya wambuzi, napanga chophimbira pamwamba pa chihemacho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaomba nsalu zophimba za ubweya wa mbuzi zikhale hema pamwamba pa Kachisi; anaomba nsalu zophimba khumi ndi imodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapanga nsalu za ubweya wambuzi zophimba pamwamba pa chihemacho. Nsalu zonse pamodzi zinalipo khumi ndi imodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaomba nsaru zophimba za ubweya wa mbuzi zikhale hema pamwamba pa kacisi; anaomba nsaru zophimba khumi ndi imodzi.