Exodus 36:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'litali mwa nsalu iliyonse munali mamita 14, ndipo muufupi mwake munali masentimita 183. Zonsezo zinali zofanana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Utali wake wa nsalu imodzi ndiwo mikono makumi atatu, ndi kupingasa kwake kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu khumi ndi imodzi zinafanana muyeso wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nsalu zonse khumi ndi imodzi zinali zofanana. Mulitali mwake munali mamita khumi ndi anayi ndipo mulifupi mwake munali mamita awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Utali wace wa nsaru imodzi ndiwo mikono makumi atatu, ndi kupingasa kwace kwa nsaru imodzi ndiko mikono inai; nsaru khumi ndi imodzi zinafanana muyeso wao.