Exodus 36:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adasokanso magonga makumi asanu m'mphepete mwake mwa nsalu yomalizira ya chinsalu choyambacho, ndi magonga ena makumi asanu m'mphepete mwa chinsalu chinacho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga magango makumi asanu m'mphepete mwa nsalu imodzi, ya kuthungo, ya chilumikizano, naika magango makumi asanu m'mphepete mwa nsalu ya kuthungo, ya chilumikizano china.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anasokerera zokolowekamo makumi asanu mʼmphepete mwa nsalu imodzi yotsirizira ya nsalu yoyamba yolumikiza ija ndiponso anapanga zokolowekamo zina makumi asanu mʼmphepete mwa nsalu yotsirizira ya nsalu inanso yolumikiza ija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga magango makumi asanu m'mphepete mwa nsaru imodzi, ya kuthungo, ya cilumikizano, naika magango makumi asanu m'mphepete mwa nsaru ya kuthungo, ya cilumikizano cina.