Exodus 36:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adapanga ngoŵe zokoŵera zokwanira makumi asanu zamkuŵa zolumikizira pamodzi nsalu ziŵirizo, kuti apange chinsalu chimodzi chophimbira chihema.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga zokowera makumi asanu zamkuwa kumanga pamodzi hemalo, kuti likhale limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapanga ngowe 50 zamkuwa zolowetsa mu zokolowekazo ndipo anaphatikiza nsalu ziwirizo kuti tentiyo ikhale imodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga zokowera makumi asanu zamkuwa kumanga pamodzi hemalo, kuti likhale limodzi.