Exodus 36:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa mbali yakumwera adapanga mafulemu makumi aŵiri,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga matabwa a Kachisi; matabwa makumi awiri a ku mbali ya kumwera, kumwera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanga maferemu makumi awiri a mbali yakummwera kwa chihemacho,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga matabwa a kacisi; matabwa makumi awiri a ku mbali ya kumwela, kumwela;