Exodus 36:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa mbali yakumpoto ya chihemacho adapanganso mafulemu makumi aŵiri
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ku mbali ina ya Kachisi, mbali ya kumpoto, anapanga matabwa makumi awiri, ndi makamwa ao makumi anai asiliva;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapanganso maferemu makumi awiri a mbali yakumpoto ya chihemacho,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ku mbali yina ya kacisi, mbali ya kumpoto, anapanga matabwa makumi awiri, ndi makamwa ao makumi anai asiliva;