Exodus 36:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndi masinde ake makumi anai asiliva, masinde aŵiri pansi pa fulemu lililonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso matsinde makumi anayi asiliva, awiri pansi pa feremu iliyonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina.