Exodus 36:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanganso mafulemu asanu ndi limodzi kumbuyo kwake kwa chihemacho chakuzambwe,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ku mbali ya kumbuyo ya Kachisi kumadzulo anapanga matabwa asanu ndi limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanganso maferemu asanu ndi imodzi a kumbuyo kwa tenti, kumbali yakumadzulo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ku mbali ya kumbuyo ya kacisi kumadzulo anapanga matabwa asanu ndi limodzi.