Exodus 36:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiponso mafulemu aŵiri am'ngodya, kumbuyo kwake kwa chihemacho.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapanganso matabwa awiri a kungodya za Kachisi, m'mbali zake ziwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndiponso maferemu awiri a pa ngodya yakumbuyo kwenikweni kwa tenti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapanganso matabwa awiri a ku ngondya za kacisi, m'mbali zace ziwirio