Exodus 36:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero panali mafulemu asanu ndi atatu, ndi masinde asiliva 16, aŵiri pansi pa fulemu lililonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali matabwa asanu ndi atatu. Ndi makamwa ao asiliva, makamwa khumi kudza asanu ndi limodzi; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho panali maferemu asanu ndi atatu ndiponso matsinde 16 asiliva, awiri anali pansi pa feremu iliyonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali matabwa asanu ndi atatu ndi makamwa ao asiliva, makamwa khumi kudza asanu ndi limodzi; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi.