Exodus 36:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kenaka adapanga mitanda ya matabwa a mtengo wa kasiya, isanu ya mafulemu a mbali imodzi ya chihema,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga mitanda ya mtengo wakasiya; isanu ya matabwa a pa mbali ina ya Kachisi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapanganso mitanda ya matabwa amtengo wa mkesha. Mitanda isanu inali ya maferemu a mbali imodzi ya chihema,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga mitanda ya mtengo wasmmu; Isanu ya matabwa a pa mbali yina ya kacisi,