Exodus 36:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
isanu ya mafulemu a mbali inayo, ndiponso isanu ya mafulemu a mbali yakuzambwe, kumbuyo kwake kwa chihema.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali inzake ya Kachisi, ndi mitanda isanu ya matabwa a Kachisi ali pa mbali ya kumadzulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mitanda isanu inanso inali ya maferemu a mbali inayo ndipo mitanda ina isanu ya mbali yakumadzulo, kumapeto kwenikweni kwa chihema.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mitanda isanu ya matabwa a pa mbali inzace ya kacisi, ndi mitanda lsanu ya matabwa a kacisi ali pa mbali ya kumadzulo.