Exodus 36:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adapanga mtanda wapakati chapakatimpakati, wogwira mafulemuwo kuyambira ku mbali imodzi ya chihema mpaka mbali ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapititsa mtanda wa pakatipo, pakati pa matabwa kufikira kuthungo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanga mtanda wapakati omwe umachokera pa maferemu a mbali ina mpaka mbali inanso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapititsa mtanda wa pakatipo, pakati pa matabwa kufikira kuthungo.