Exodus 36:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimene anali atazisonkhanitsa zidachuluka kuposa zimene zinkafunika kuti amalize ntchitoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza zipangizo zinakwanira ntchito yonse ichitike, zinatsalakonso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa zimene anali nazo zinali zoposera zimene zimafunika kugwirira ntchito yonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza zipangizo zinakwanira nchito yonse icitike, zinatsalakonso.