Exodus 37:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Bezalele adapanga bokosi lachipangano ndi matabwa a mtengo wa kasiya. Kutalika kwake kunali masentimita 114, muufupi mwake masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Bezalele anapanga likasa la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwake mkono ndi hafu, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bezaleli anapanga Bokosi la Chipangano lamatabwa amtengo wa mkesha. Kutalika kwake kunali masentimita 114, mulifupi mwake munali masentimita 69, msinkhu wake masentimita 69.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Bezaleli anapanga likasa la mtengo wasitimu; utali wace mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwace mkono ndi hafu, ndi msinkhu wace mkono ndi hafu;