Exodus 37:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bezalele adapanganso tebulo la matabwa a mtengo wa kasiya, m'litali mwake masentimita 91, muufupi mwake masentimita 46, ndipo mumsinkhu mwake masentimita 69,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga gome la mtengo wakasiya; utali wake mikono iwiri, ndi kupingasa kwake mkono umodzi, ndi msinkhu wake mkono ndi hafu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapanga tebulo la matabwa amtengo wa mkesha, mulitali mwake masentimita 91, mulifupi mwake masentimita 46, msinkhu wake masentimita 69.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga gome la mtengo wasitimu; utali wace mikono iwiri, ndi kupingasa kwace mkono limodzi, ndi msinkhu wace mkono ndi hafu;