Exodus 37:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanga mphiko za matabwa a mtengo wa kasiya, nazikuta ndi golide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi golide, kunyamulira nazo gomelo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanga nsichi zamtengo wa mkesha ndi kuzikuta ndi golide kuti azinyamulira tebulolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga mphiko za mtengo wasitimu, nazikuta ndigolidi, kunyamulira nazo gomelo.