Exodus 37:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa mbali zake adapanga nthambi zisanu ndi imodzi, zitatu pa mbali iliyonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi m'mbali zake munatuluka mphanda zisanu ndi imodzi; mphanda zitatu za choikapo nyali zotuluka m'mbali yake imodzi, ndi mphanda zitatu za choikapo nyali zotuluka m'mbali yake ina;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼmbali mwake munali mphanda zisanu ndi imodzi, zitatu mbali iliyonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi m'mbali zace munaturuka mphanda zisanu ndi imodzi; mphanda zitatu za coikapo nyali zoturuka m'mbali yace imodzi, ndi mphanda zitatu za coikapo nyali zoturuka m'mbali yace yina;