Exodus 37:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa thunthu lake la choikaponyalecho panali zikho zinai zonga maluŵa amtowo okhala ndi nkhunje zake ndi maluŵa ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pa choikapo nyali chomwe panali zikho zinai zopangika ngati katungurume, mitu yake ndi maluwa ake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa choyikapo nyalecho panali zikho zinayi zokhala ngati maluwa amtowo, mphukira ndi maluwa ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pa coikapo nyali comwe panali zikho zinai zopangika ngati katungurume, mitu yace ndi maluwa ace;