Exodus 37:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popanga choikaponyalecho, pamodzi ndi zipangizo zake zonsezo, adagwiritsa ntchito makilogaramu 34 a golide wabwino kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anachipanga ichi ndi zipangizo zake zonse za talente wa golide woona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapanga choyikapo nyale ndi zipangizo zake zonse zagolide wabwino kwambiri wolemera makilogalamu 34.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anacipanga ici ndi zipangizo zace zonse za talente wa golidi woona.