Exodus 37:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanga mphiko zinai za matabwa a mtengo wa kasiya, nazikuta ndi golide,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi golide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anapanga mizati yamtengo wa mkesha ndi kuzikuta ndi golide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga mphiko za mtengo wasitimu, nazikuta ndi golidi.