Exodus 38:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa mbali inayo yakuvuma panalinso mamita 23.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pa mbali ya kum'mawa, kum'mawa, mikono makumi asanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbali yakummawa, kotulukira dzuwa, inalinso yotalika mamita 23.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pa mbali ya kum'mawa, kum'mawa, mikono makumi asanu.