Exodus 38:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa mbali inayo panali chimodzimodzi. Choncho pa mbali zonse ziŵirizo za chipata choloŵera ku bwalo chija, panali nsalu zochinga, zotalika mamita asanu ndi aŵiri, zokhala ndi nsanamira zitatu ndi masinde atatu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
momwemonso pa mbali ina: pa mbali yino ndi pa mbali ina ya chipata cha pabwalo panali nsalu zochingira za mikono khumi ndi isanu; nsichi zake zitatu, ndi makamwa ake atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
polowera mʼbwalo panali nsalu yotchinga ya mamita asanu ndi awiri pamodzi ndi mizati itatu ndi matsinde atatu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
momwemonso pa mbali yina: pa mbali yino ndi pa mbali yina ya cipata ca pabwalo panali nsaru zocingira za mikono khumi ndi isanu; nsici zace zitatu, ndi makamwa ace atatu.