Exodus 38:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nsalu zonse zochinga kuzungulira bwalolo zinali za bafuta wosalala ndi wopikidwa bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nsalu zochingira zonse za pabwalo pozungulira zinali za bafuta wa thonje losansitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Katani yonse yotchinga kuzungulira chihema inali yofewa, yosalala ndi yolukidwa bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nsaru zocingira zonse za pabwalo pozungulira zinali za bafuta wa thonje losansitsa.