Exodus 38:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nsaluzo adazikoloŵeka ku nsanamira zinai zokhala m'masinde anai amkuŵa. Ngoŵe za pa nsanamira, mitu yake ndi mitanda yake, zonsezo zinali zasiliva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi nsichi zake zinali zinai, ndi makamwa ake anai, amkuwa; zokowera zake zasiliva, ndi zokutira mitu yake ndi mitanda yake zasiliva.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamodzi ndi mizati yake inayi ndi matsinde amkuwa anayi. Ngowe ndi zingwe zake zinali za siliva, ndipo pamwamba pake pa mzati anakutapo ndi siliva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi nsici zace zinali zinai, ndi makamwa ace anai, amkuwa; zokowera zace zasiliva, ndi zokutira mitu yace ndi mitanda yace zasiliva.