Exodus 38:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa ngodya zake zinai adapangapo nyanga zotuluka m'guwalo, mwakuti zidangolumikizika nkukhala chinthu chimodzi ndi guwalo. Ndipo guwa lonselo adalikuta ndi mkuŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga nyanga zake pangodya zake zinai; nyanga zake zinakhala zotuluka m'mwemo; ndipo analikuta ndi mkuwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanga nyanga imodziimodzi pa ngodya zake zinayizo, kotero kuti nyangazo ndi guwalo zinali chinthu chimodzi, ndipo anakuta guwalo ndi mkuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga nyanga zace pa ngondya zace zinai; nyanga zace zinakhala zoturuka m'mwemo; ndipo analikuta ndi mkuwa.