Exodus 38:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Siliva wochokera kwa mpingo wonse wa anthu, anali wolemera makilogaramu 3,430, potsata miyeso ya ku Nyumba ya Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo siliva wa iwo owerengedwa a khamulo ndiwo matalente zana limodzi, ndi masekeli chikwi chimodzi, kudza mazana asanu ndi awiri, mphambu makumi asanu ndi awiri kudza asanu, kuyesa sekeli wa malo opatulika;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Siliva wochokera ku gulu lonse la anthu anali wolemerera makilogalamu 3,430, potsata miyeso ya ku malo wopatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo siliva wa iwo owerengedwa a khamulo ndiwo matalente zana limodzi, ndi masekeli cikwi cimodzi, kudza mazana asanu ndi awiri, mphambu makumi asanu ndi awiri kudza asanu, kuyesa sekeli wa malo opatulika;