Exodus 38:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkuŵa umene adaapereka kwa Chauta udakwana makilogaramu 2,425 pamodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi mkuwa wa choperekacho ndiwo matalente makumi asanu ndi awiri, ndi masekeli zikwi ziwiri kudza mazana anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkuwa ochokera ku nsembe yoweyula unali makilogalamu 2,425.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mkuwa wa coperekaco ndiwo matalente makumi asanu ndi awiri, ndi masekeli zikwi ziwiri kudza mazana anai.