Exodus 38:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndi mkuŵa umenewu adapanga masinde a pa chipata choloŵera ku chihema chamsonkhano. Adapanganso guwa la nsembe zopsereza, pamodzi ndi chitsulo cha sefa, zipangizo zonse za guwalo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga nao makamwa a pa khomo la chihema chokomanako, ndi guwa la nsembe lamkuwa, ndi sefa wake amkuwa, ndi zipangizo zonse za guwa la nsembe,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anawugwiritsa ntchito popanga matsinde a pa chipata cha tenti ya msonkhano, guwa la mkuwa pamodzi ndi sefa yake ndiponso ziwiya zonse,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga nao makamwa a pa khomo la cihema cokomanako, ndi guwa la nsembe lamkuwa, ndi made ace amkuwa, ndi zipangizo zonse za guwa la nsembe,