Exodus 38:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adasema mphiko zonyamulira za mtengo wa kasiya, nazikuta ndi mkuŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Napanga mphiko za mtengo wakasiya, nazikuta ndi mkuwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanga nsichi zamtengo wa mkesha ndipo anazikuta ndi mkuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Napanga mphiko za mtengo wasitimu, nazikuta ndi mkuwa.