Exodus 38:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adapanga bwalo. Nsalu zake zochingira bwalolo chakumwera kwake zinali za bafuta wosalala ndi wopikidwa bwino, ndipo kutalika kwake kunali mamita 46.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga bwalo; pa mbali ya kumwera, kumwera, nsalu zochingira za pabwalo zinali za bafuta wa thonje losansitsa, mikono zana limodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anapanga bwalo la chihema. Mbali yakummwera inali yotalika mamita 46 ndipo kunali nsalu yotchinga yofewa yosalala yolukidwa bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga bwalo; pa mbali ya kumwela, kumwela, nsaru zocingira za pabwalo zinali za bafuta wa thonje losansitsa, mikono zana limodzi;