Exodus 39:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanga timaunyolo ta chovala chapachifuwa ta golide wabwino kwambiri, topota mwaluso ngati maukufu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapangira pachapachifuwa maunyolo ngati zingwe, ntchito yopota ya golide woona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanga timaunyolo tagolide wabwino kwambiri ta pa chovala chapachifuwa, topota ngati chingwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapangira pacapacifuwa maunyolo ngati zingwe, nchito yopota ya golidi woona.