Exodus 39:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanga mphete ziŵiri zagolide, nazilumikiza ku nsonga ziŵiri za chovala chapachifuwa cham'mphepete, m'kati mwake, pafupi ndi chovala cha efodi chija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga mphete ziwiri zagolide, naziika pa nsonga ziwiri za chapachifuwa, m'mphepete mwake m'katimo, pa mbali ya kuefodi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanganso mphete ziwiri zagolide ndipo analumikiza ku ngodya ziwiri zamʼmunsi mwa chovala chapachifuwa, champhepete mwake, mʼkati pafupi ndi efodi ija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga mphete ziwiri zagolidi, naziika pa nsonga ziwiri za capacifuwa, m'mphepete mwace m'katimo, pa mbali ya kuefodi.