Exodus 39:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanga chovala chopatulika cha efodi ndi nsalu yagolide ndiponso ndi nsalu yobiriŵira, yofiirira ndi yofiira, ndi ya bafuta wosalala ndi wopikidwa bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaomba efodi wa golide, lamadzi, lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popanga efodi, iwo anagwiritsa ntchito golide, nsalu yamtundu wa mtambo, yapepo, yofiira, yosalala yofewa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaomba efodi wa golidi, lamadzi, lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa.