Exodus 39:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkanjowo unali ndi popisa mutu, ndipo maonekedwe ake anali ngati popisa mutu pa malaya. M'mbali mwake kuzungulira, munali mosokerera bwino, kuti ungang'ambike.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi pakati pake polowa mutu, ngati polowa pa malaya ochingirizira, ndipo anabinyira pozungulira polowa pake, pangang'ambike.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkanjowo unali ndi malo opisapo mutu pakati pakepo. Pa chibowopo panali chibandi chosokedwa mochita ngati kuluka monga muja akhalira malaya kuti chibowocho chilimbe, chisangʼambike.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi pakati pace polowa mutu, ngati polowa pa maraya ocingirizira, ndipo anabinyira pozungulira polowa pace, pangang'ambike.