Exodus 39:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Aroni ndi ana ake, amisiri aja adaŵapangira miinjiro,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaomba malaya a bafuta, a ntchito yoomba, a Aroni, ndi a ana ake amuna,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa Aaroni ndi ana ake anawapangira minjiro ya nsalu yofewa yosalala, yolukidwa bwino ndi munthu waluso,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaomba maraya a bafuta, a nchito yoomba, a Aroni, ndi a ana ace amuna,