Exodus 39:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapanganso lamba wa bafuta wosalala ndi wopikidwa bwino ndi wa thonje lobiriŵira, lofiira ndi lofiirira, ndipo adamkongoletsa ndi zopetapeta, monga momwe Chauta adalamulira Mose.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mpango wabafuta wa thonje losansitsa, ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ntchito ya wopikula; monga Yehova adamuuza Mose.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapanga lamba wolukidwa bwino wa nsalu yofewa ndi yosalala ya mtundu wa mtambo yapepo ndi yofiira. Ili linaliluso la munthu wopanga zokometsera monga Yehova analamulira Mose.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mpango wabafuta wa thonje losansitsa, ndi lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, nchito ya wopikula; monga Yehova adamuuza Mose.