Exodus 39:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adapanga duŵa la golide wabwino kwambiri. Limenelo linali chizindikiro chopatulika, ndipo mofanizira ndi mazokotedwe a chidindo, adazokotapo mau akuti, “Chopereka kwa Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapanga phanthiphanthi wa korona wopatulika wa golide woona, nalembapo lemba, ngati malochedwe a chosindikizira, KUPATULIKIRA YEHOVA.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapanga duwa lagolide wabwino kwambiri ngati chidindo ndipo anazokotapo mawu akuti, WOPATULIKIRA YEHOVA.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapanga phanthiphanthi wa korona wopatulika wa golidi woona, nalembapo lemba, ngati malocedwe a cosindikizira, KUPATULIKIRA YEHOVA.