Exodus 39:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adapanga tizikwewo tam'mapewa ta chovala cha efodi chija, tolumikizika ku chovalacho pa mbali zake ziŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapangira efodi zapamapewa zolumikizana; pa nsonga ziwirizo anamlumikiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapanga efodi imene inali ndi timalamba tiwiri ta pa mapewa, tosokerera ku msonga zake ziwiri kuti azitha kumanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapangira efodi zapamapewa zolumikizana; pa nsonga ziwirizo anamlumikiza.