Exodus 39:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kutalika kwake kwa chovala chapachifuwacho kunali masentimita 23, muufupi mwakenso masentimita 23, ndipo chinali chopinda paŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinakhala chaphwamphwa; anachiomba chapachifuwa chopindika; utali wake dzanja limodzi, ndi kupingasa kwake dzanja limodzi, chinakhala chopindika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kutalika kwake kunali kofanana mbali zonse, mulitali masentimita 23, mulifupi masentimita 23, chinali chopinda pawiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinakhala camowamphwa; anaciomba capacifuwa copindika; utali wace cikhato cimodzi, ndi kupingasa kwace cikhato cimodzi, cinakhala copindika.