Exodus 4:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adauza Mose ku Midiyani kuja kuti, “Bwerera ku Ejipito tsopano popeza kuti onse aja ankafuna kukuphaŵa adamwalira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'Midiyani, Muka, bwerera kunka ku Ejipito; pakuti adafa anthu onse amene anafuna moyo wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawiyi Yehova anali atamuwuza kale Mose ku Midiyani kuti, “Bwerera ku Igupto, pakuti anthu onse amene amafuna kukupha aja anamwalira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'Midyani, Muka, bwerera kumka ku Aigupto; pakuti adafa anthu onse amene anafuna moyo wako.