Exodus 4:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho ndikukuuza kuti umlole mwana wanga apite akandipembedze Ine. Tsono iweyo ukakana, Ine ndidzapha mwana wako wamwamuna wachisamba.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndanena ndi iwe, Mlole mwana wanga amuke, kuti anditumikire Ine; koma wakana kumlola kuti asamuke; taona, Ine ndidzamupha mwana wako wamwamuna, mwana wako woyamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ndikuti, ‘Mulole mwana wanga apite kuti akandipembedze. Koma ngati ukana, Ine ndidzapha mwana wako wachisamba.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndanena ndi iwe, Mlole mwana wanga amuke, kuti anditumikire Ine; koma wakana kumlola kuti asamuke; taona, Ine ndidzamupha mwana wako wamwamuna, mwana wako woyamba.